Mateyu 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+ Maliko 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+ Luka 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+
21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+
17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+
2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+