Mateyu 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi pamenepa, pouka kwa akufa, mkazi ameneyu adzakhala wa ndani popeza onse 7 anamukwatira?”+ Maliko 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi pouka kwa akufa mkazi ameneyu adzakhala wa ndani? Popeza onse 7 anam’kwatira.”+