Mateyu 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amakonda malo olemekezeka kwambiri+ pa chakudya chamadzulo ndi mipando yakutsogolo m’masunagoge.+ Maliko 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Komanso amakonda kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+
39 Komanso amakonda kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+