Mateyu 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndikukuuzani kuti kumwamba ndi dziko lapansi zingachoke mosavuta,+ kusiyana n’kuti kalemba kochepetsetsa kapena kachigawo kamodzi ka lemba kachoke m’Chilamulo zinthu zonse zisanachitike.+
18 Ndithu ndikukuuzani kuti kumwamba ndi dziko lapansi zingachoke mosavuta,+ kusiyana n’kuti kalemba kochepetsetsa kapena kachigawo kamodzi ka lemba kachoke m’Chilamulo zinthu zonse zisanachitike.+