Mateyu 24:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka,+ koma mawu anga sadzachoka ayi.+ Luka 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndithudi, n’chapafupi kuti kumwamba ndi dziko lapansi zichoke+ kusiyana n’kuti ngakhale mbali chabe ya chilembo chimodzi+ cha m’Chilamulo isakwaniritsidwe.+ Luka 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka,+ koma mawu anga sadzachoka ayi.+
17 Ndithudi, n’chapafupi kuti kumwamba ndi dziko lapansi zichoke+ kusiyana n’kuti ngakhale mbali chabe ya chilembo chimodzi+ cha m’Chilamulo isakwaniritsidwe.+