1 Mafumu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo ukayenda+ pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, yemwe anali ndi mtima wosagawanika+ ndipo anayenda mowongoka,+ ukachita mogwirizana ndi zonse zimene ndinakulamula,+ komanso ukasunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+ 2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ Salimo 119:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo sindikanachita manyazi,+Pamene ndikulabadira malamulo anu onse.+
4 Iweyo ukayenda+ pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, yemwe anali ndi mtima wosagawanika+ ndipo anayenda mowongoka,+ ukachita mogwirizana ndi zonse zimene ndinakulamula,+ komanso ukasunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+