Yohane 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+ 1 Petulo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye sanachite tchimo,+ ndipo m’kamwa mwake simunapezeke chinyengo.+
38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+