Aheberi 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’malomwake, zimangokhudza zakudya,+ zakumwa,+ ndi miyambo yosiyanasiyana yoviika zinthu m’madzi.+ Zimenezo zinali zofunika za Chilamulo zokhudza zinthu zathupi,+ ndipo zinakhazikitsidwa kufikira nthawi yoikidwiratu yokonzanso zinthu.+
10 M’malomwake, zimangokhudza zakudya,+ zakumwa,+ ndi miyambo yosiyanasiyana yoviika zinthu m’madzi.+ Zimenezo zinali zofunika za Chilamulo zokhudza zinthu zathupi,+ ndipo zinakhazikitsidwa kufikira nthawi yoikidwiratu yokonzanso zinthu.+