Maliko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo iwo anafuula kuti: “M’pachikeni!”+ Yohane 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+
6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+