Yohane 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo Pilato anati: “M’tengeni eniakenu mukamuweruze mogwirizana ndi chilamulo chanu.”+ Ayudawo anati: “N’zosaloleka kwa ife kupha munthu aliyense.”+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
31 Pamenepo Pilato anati: “M’tengeni eniakenu mukamuweruze mogwirizana ndi chilamulo chanu.”+ Ayudawo anati: “N’zosaloleka kwa ife kupha munthu aliyense.”+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+