Mateyu 27:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ameneyutu ndi Mfumu+ ya Isiraeli, atsiketu pamtengo wozunzikirapowo kuti ife timukhulupirire.+ Maliko 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chimodzimodzinso ansembe aakulu. Nawonso anali kumuchita chipongwe limodzi ndi alembi. Iwo anali kunena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikum’kanika!+
42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ameneyutu ndi Mfumu+ ya Isiraeli, atsiketu pamtengo wozunzikirapowo kuti ife timukhulupirire.+
31 Chimodzimodzinso ansembe aakulu. Nawonso anali kumuchita chipongwe limodzi ndi alembi. Iwo anali kunena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikum’kanika!+