40 Panali amayi amene anali kuonerera chapatali ndithu,+ ena mwa iwo anali Mariya Mmagadala, Mariya mayi wa Yakobo Wamng’ono ndi Yose, komanso Salome,+
2 Analinso ndi amayi+ ena amene anawatulutsa mizimu yoipa ndi kuwachiritsa matenda awo. Ena mwa iwo anali Mariya wotchedwanso Mmagadala, amene anamutulutsa ziwanda 7.+