Mateyu 27:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Mariya Mmagadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+ Maliko 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Mariya Mmagadala ndi Mariya mayi wa Yose, anali kuyang’anitsitsa pamene anaikidwapo.+