1 Timoteyo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mkazi amene alidi wamasiye, amene akusowa womusamala,+ amadalira Mulungu+ ndipo amalimbikira mapembedzero ndi mapemphero usiku ndi usana.+
5 Mkazi amene alidi wamasiye, amene akusowa womusamala,+ amadalira Mulungu+ ndipo amalimbikira mapembedzero ndi mapemphero usiku ndi usana.+