Luka 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero. Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse, osaleka.+
37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.