Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Mateyu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’” Maliko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova* anthu inu, wongolani misewu yake,’”+
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’”
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova* anthu inu, wongolani misewu yake,’”+