Maliko 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Monga mmene analembera m’buku la mneneri Yesaya kuti: “(Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga pamaso pako, amene adzakonza njira yako.)*+ Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+
2 Monga mmene analembera m’buku la mneneri Yesaya kuti: “(Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga pamaso pako, amene adzakonza njira yako.)*+
23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+