1 Samueli 17:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, bambo wako ndani?” Poyankha Davide anati: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+ Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+ Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, bambo wako ndani?” Poyankha Davide anati: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+