Rute 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Boazi anatenga Rute kukhala mkazi wake ndipo anagona naye. Pamenepo Yehova anam’dalitsa ndipo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna.
13 Choncho Boazi anatenga Rute kukhala mkazi wake ndipo anagona naye. Pamenepo Yehova anam’dalitsa ndipo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna.