Genesis 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano iyi ndi mbiri ya Tera. Tera anabereka Abulamu, Nahori ndi Harana. Harana anabereka Loti.+ 1 Mbiri 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a Abulahamu anali Isaki+ ndi Isimaeli.+ Mateyu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi abale ake.