Mateyu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina wotchedwa Mateyu atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Nthawi yomweyo ananyamuka ndi kum’tsatira.+ Maliko 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pamene anali kudutsa, anaona Levi+ mwana wa Alifeyo, atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Pamenepo Levi ananyamuka ndi kumutsatira.+
9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina wotchedwa Mateyu atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Nthawi yomweyo ananyamuka ndi kum’tsatira.+
14 Koma pamene anali kudutsa, anaona Levi+ mwana wa Alifeyo, atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Pamenepo Levi ananyamuka ndi kumutsatira.+