Mateyu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene anali kufesa, mbewu zina zinagwera m’mbali mwa msewu, ndipo kunabwera mbalame ndi kuzidya.+ Maliko 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene anali kufesa, mbewu zina zinagwera m’mbali mwa msewu, ndipo kunabwera mbalame ndi kuzidya.+ Luka 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zogwera m’mbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo.+ Kenako Mdyerekezi+ amabwera ndi kudzachotsa mawuwo m’mitima yawo kuti asakhulupirire ndi kupulumuka.+
12 Zogwera m’mbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo.+ Kenako Mdyerekezi+ amabwera ndi kudzachotsa mawuwo m’mitima yawo kuti asakhulupirire ndi kupulumuka.+