Mateyu 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+ Maliko 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbewu zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+ Luka 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira ndi chimwemwe, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+
5 Zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+
5 Mbewu zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+
13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira ndi chimwemwe, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+