Mateyu 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kuwauza zimenezi, wolamulira wina+ anam’yandikira. Kenako anamugwadira+ n’kunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale.+ Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+ Maliko 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndi kum’chonderera mobwerezabwereza, kuti: “Mwana wanga wamkazi akudwala mwakayakaya. Chonde tiyeni mukamuike manja+ kuti achire ndi kukhala ndi moyo.”+
18 Pamene anali kuwauza zimenezi, wolamulira wina+ anam’yandikira. Kenako anamugwadira+ n’kunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale.+ Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+
23 ndi kum’chonderera mobwerezabwereza, kuti: “Mwana wanga wamkazi akudwala mwakayakaya. Chonde tiyeni mukamuike manja+ kuti achire ndi kukhala ndi moyo.”+