Numeri 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi tiwaphera ziweto zonse kuti ziwakwanire?+ Kapena tiwaphera nsomba zonse za m’nyanja kuti ziwakwanire?” Salimo 78:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+
22 Kodi tiwaphera ziweto zonse kuti ziwakwanire?+ Kapena tiwaphera nsomba zonse za m’nyanja kuti ziwakwanire?”
19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+