Maliko 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ophunzirawo sanali kumvetsa mawuwa, ndipo anali kuopa kumufunsa.+ Luka 2:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma iwo sanamvetse zimene anali kuwauzazo.+