Luka 9:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+ Luka 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iwo sanamvetse tanthauzo la chilichonse cha zimenezi. Mawu amenewa anabisika kwa iwo, ndipo sanadziwe zimene zinanenedwazo.+
45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+
34 Koma iwo sanamvetse tanthauzo la chilichonse cha zimenezi. Mawu amenewa anabisika kwa iwo, ndipo sanadziwe zimene zinanenedwazo.+