Mateyu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma wamkulu kwambiri pakati panu akhale mtumiki wanu.+ Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.