Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+

  • Nehemiya 9:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ngakhale kuti munali kuwalimbikitsa+ kuti abwerere ku chilamulo chanu,+ iwo anali kuchita zinthu modzikuza+ ndipo sanali kumva malamulo anu. Anachimwira zigamulo zanu,+ zimene ngati munthu azitsatira adzakhala ndi moyo chifukwa cha zigamulozo.+ Iwo anatseka makutu*+ awo ndi kuumitsa khosi+ lawo ndipo sanamvere.+

  • Ezekieli 20:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “‘“Kumeneko ndinawapatsa malamulo+ ndi kuwadziwitsa zigamulo zanga,+ kuti munthu amene akuzitsatira akhalebe ndi moyo.+

  • Yohane 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+

  • Aroma 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pajatu Mose analemba kuti munthu wochita chilungamo cha m’Chilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilungamo chimenecho.+

  • Agalatiya 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano, Chilamulo sichidalira chikhulupiriro, koma “wochita za m’Chilamulo adzakhala ndi moyo potsatira chilamulocho.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena