Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+ Luka 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo ngakhale tsitsi+ lonse la m’mutu mwanu analiwerenga. Musachite mantha. Ndinu ofunika kwambiri kuposa mpheta zambiri.+
26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+
7 Ndipo ngakhale tsitsi+ lonse la m’mutu mwanu analiwerenga. Musachite mantha. Ndinu ofunika kwambiri kuposa mpheta zambiri.+