Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya? Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+ Mateyu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi mpheta ziwiri si paja amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu?+ Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+ Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+
41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?
29 Kodi mpheta ziwiri si paja amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu?+ Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+
24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+