2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+ Yesaya 65:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo asanandiitane, ine ndidzayankha.+ Asanamalize kulankhula, ine ndidzamva.+ Mateyu 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti anthu a mitundu ina akufunafuna mwakhama zinthu zonsezi. Koma Atate wanu wakumwamba akudziwa kuti inuyo mumafunikira zinthu zonsezi.+ Afilipi 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.
9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+
32 Pakuti anthu a mitundu ina akufunafuna mwakhama zinthu zonsezi. Koma Atate wanu wakumwamba akudziwa kuti inuyo mumafunikira zinthu zonsezi.+
19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.