Yesaya 58:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+ Luka 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+ Aroma 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu+ umatithandiza pa zofooka zathu.+ Pakuti chimene tiyenera kupempherera monga mmene tiyenera kupemphera sitikuchidziwa,+ koma mzimu+ umachonderera m’malo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.
9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+
30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+
26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu+ umatithandiza pa zofooka zathu.+ Pakuti chimene tiyenera kupempherera monga mmene tiyenera kupemphera sitikuchidziwa,+ koma mzimu+ umachonderera m’malo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.