Mateyu 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse. Maliko 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako panafika mkazi wamasiye wosauka ndipo anaponyamo timakobidi tiwiri tating’ono.+
34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse.