9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+
13 anatenga nthambi za kanjedza+ ndi kutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti:+ “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova,+ amenenso ndi mfumu+ ya Isiraeli!”