Mateyu 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amakonda malo olemekezeka kwambiri+ pa chakudya chamadzulo ndi mipando yakutsogolo m’masunagoge.+ Luka 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsoka inu Afarisi, chifukwa mumakonda mipando yakutsogolo m’masunagoge ndi kupatsidwa moni m’misika!+ Luka 20:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Chenjerani ndi alembi. Iwo amakonda kuyendayenda atavala mikanjo. Amakonda kupatsidwa moni m’misika ndi kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+
43 Tsoka inu Afarisi, chifukwa mumakonda mipando yakutsogolo m’masunagoge ndi kupatsidwa moni m’misika!+
46 “Chenjerani ndi alembi. Iwo amakonda kuyendayenda atavala mikanjo. Amakonda kupatsidwa moni m’misika ndi kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+