Genesis 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu atamva zimenezi anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo amene adzakhale wolowa nyumba yanga ndi munthu wa ku Damasiko, Eliezere.”+ Genesis 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+
2 Abulamu atamva zimenezi anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo amene adzakhale wolowa nyumba yanga ndi munthu wa ku Damasiko, Eliezere.”+
2 Chotero Abulahamu anauza mtumiki wake yemwe anali wamkulu koposa m’nyumba yake, ndi woyang’anira zinthu zake zonse,+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+