Mateyu 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “N’chifukwa chake ufumu wakumwamba uli ngati mfumu+ imene inafuna kuti akapolo ake abweze ngongole.+ Mateyu 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Patapita nthawi yaitali,+ mbuye wa akapolowo anabwera ndi kuwerengerana nawo ndalama.+ 1 Petulo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu amenewa adzayankha mlandu kwa yemwe ali+ wokonzeka kuweruza amoyo ndi akufa.+
23 “N’chifukwa chake ufumu wakumwamba uli ngati mfumu+ imene inafuna kuti akapolo ake abweze ngongole.+