Mlaliki 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tumiza mkate wako+ pamadzi,+ chifukwa pakapita masiku ambiri udzaupezanso.+ Luka 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+
8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+