Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero pamene ukupereka mphatso zachifundo,+ usalize lipenga+ muja amachitira onyenga m’masunagoge ndi m’misewu, kuti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.

  • Mateyu 23:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.

  • Luka 10:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma pofuna kudzionetsa kuti ndi wolungama, munthuyo anafunsa Yesu kuti: “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?”+

  • Luka 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yesu ananenanso fanizo lotsatirali kwa ena odzidalira, odziona ngati olungama+ amenenso amaona ena onse ngati opanda pake.+ Iye anati:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena