Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala+ kwenikweni kumene kumaunikira+ anthu osiyanasiyana+ kunali pafupi kubwera m’dziko. Yohane 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.” Yohane 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene ine ndili m’dziko, ndine kuwala kwa dzikoli.”+ Yohane 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndabwera monga kuwala m’dziko,+ kuti aliyense wokhulupirira ine asapitirize kukhala mumdima.+
12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.”