Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 8:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+

  • Yohane 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+

  • Yohane 18:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pamenepo Pilato anati: “Chabwino, koma kodi ndiwe mfumu?” Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha kuti ndine mfumu.+ Chimene ndinabadwira, ndiponso chimene ndinabwerera m’dziko, ndicho kudzachitira umboni choonadi.+ Aliyense amene ali kumbali ya choonadi+ amamvera mawu anga.”+

  • 2 Akorinto 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena