Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+ Maliko 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atangovuuka m’madzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka, ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+ Luka 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba, akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+
16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+
10 Atangovuuka m’madzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka, ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+
22 Pamenepo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba, akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+