Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndinene za lamulo la Yehova.

      Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+

      Lero, ine ndakhala bambo ako.+

  • Mateyu 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+

  • Maliko 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+

  • Yohane 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Yohane anachitiranso umboni kuti: “Ndinaona mzimu ukutsika ngati nkhunda kuchokera kumwamba, ndipo unakhalabe pa iye.+

  • 2 Petulo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena