Mateyu 26:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, Yudasi,+ mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi khamu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga+ ndi zibonga.+ Maliko 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka ndi kupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+ Luka 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Koma Yesu anamufunsa kuti: “Yudasi, kodi ukupereka Mwana wa munthu mwa kupsompsona?”+ Yohane 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Popeza kuti Yudasi anali kusunga bokosi la ndalama,+ ena anali kuganiza kuti Yesu anali kumuuza kuti: “Ugule zofunikira zonse za chikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.+ Machitidwe 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+
47 Mawu adakali m’kamwa, Yudasi,+ mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi khamu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga+ ndi zibonga.+
10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka ndi kupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+
29 Popeza kuti Yudasi anali kusunga bokosi la ndalama,+ ena anali kuganiza kuti Yesu anali kumuuza kuti: “Ugule zofunikira zonse za chikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.+
16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+