-
Machitidwe 16:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chotero tinanyamuka ulendo wa panyanja kuchokera ku Torowa. Tinayenda molunjika mpaka ku Samatirake, koma tsiku lotsatira tinafika ku Neapoli.
-