Akolose 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso Arikipo+ mumuuze kuti: “Uonetsetse kuti utumiki umene unaulandira mwa Ambuye ukuukwaniritsa.” 1 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+ 1 Timoteyo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+
17 Komanso Arikipo+ mumuuze kuti: “Uonetsetse kuti utumiki umene unaulandira mwa Ambuye ukuukwaniritsa.”
2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+
16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+