2 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu. 1 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mogwirizana ndi zimenezi, inu mukudziwa bwino mmene tinali kudandaulira kwa aliyense wa inu, monga mmene bambo+ amachitira ndi ana ake, kukulimbikitsani+ ndi kukuchondererani,
4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikusautsika ndi kuzunzika kwambiri mumtima, pamodzi ndi misozi yambiri,+ osati kuti muchite chisoni,+ koma kuti mudziwe chikondi chimene ndili nacho makamaka pa inu.
11 Mogwirizana ndi zimenezi, inu mukudziwa bwino mmene tinali kudandaulira kwa aliyense wa inu, monga mmene bambo+ amachitira ndi ana ake, kukulimbikitsani+ ndi kukuchondererani,