Deuteronomo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+ Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+ Akolose 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 komanso muziyamika Atate, amene anakuyeneretsani kuti mupatsidweko gawo pa cholowa+ cha oyerawo,+ amene ali m’kuwala.+
3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+
18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+
12 komanso muziyamika Atate, amene anakuyeneretsani kuti mupatsidweko gawo pa cholowa+ cha oyerawo,+ amene ali m’kuwala.+