Machitidwe 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera Baranaba ndi Paulo pamene anali kufotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo pakati pa anthu a mitundu ina.+ Aroma 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti sindidzayesa m’pang’ono pomwe kulankhula kanthu ngakhale kamodzi kokha ngati sikanachokere m’zinthu zimene Khristu anachita mwa ine+ kuti mitundu ina ikhale yomvera.+ Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu anga+ ndi zochita zanga,
12 Pamenepo gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera Baranaba ndi Paulo pamene anali kufotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo pakati pa anthu a mitundu ina.+
18 Pakuti sindidzayesa m’pang’ono pomwe kulankhula kanthu ngakhale kamodzi kokha ngati sikanachokere m’zinthu zimene Khristu anachita mwa ine+ kuti mitundu ina ikhale yomvera.+ Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu anga+ ndi zochita zanga,